-
Deuteronomo 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mizinda yonseyi inali yamipanda yolimba yomwe inali ndi makoma aatali, zitseko ndiponso mipiringidzo. Tinalandanso matauni ambirimbiri akumidzi.
-