-
Deuteronomo 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mizinda yonseyi inali ya mipanda yolimba kwambiri ndiponso yaitali, yokhala ndi zitseko ndi mipiringidzo. Kuwonjezera pamenepo, tinalandanso matauni ambirimbiri akumidzi.
-