Deuteronomo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 mpaka Yehova atapereka mpumulo kwa abale anu, ngati mmene wachitira ndi inu ndiponso mpaka iwo atatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akuwapatsa tsidya linalo la Yorodano. Mukatero mudzabwerera, aliyense kumalo ake amene ndakupatsani.’+
20 mpaka Yehova atapereka mpumulo kwa abale anu, ngati mmene wachitira ndi inu ndiponso mpaka iwo atatenga dziko limene Yehova Mulungu wanu akuwapatsa tsidya linalo la Yorodano. Mukatero mudzabwerera, aliyense kumalo ake amene ndakupatsani.’+