Deuteronomo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa nthawi imeneyo ndinalamula Yoswa+ kuti: ‘Iwe waona ndi maso ako zonse zimene Yehova Mulungu wanu wachitira mafumu awiriwa. Yehova adzachitanso chimodzimodzi ndi maufumu onse amene ali kumene mukuwolokera kukamenyana nawo.+
21 Pa nthawi imeneyo ndinalamula Yoswa+ kuti: ‘Iwe waona ndi maso ako zonse zimene Yehova Mulungu wanu wachitira mafumu awiriwa. Yehova adzachitanso chimodzimodzi ndi maufumu onse amene ali kumene mukuwolokera kukamenyana nawo.+