Deuteronomo 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula Yoswa+ kuti, ‘Iwe ukuona ndi maso zonse zimene Yehova Mulungu wanu wachita ndi mafumu awiriwa. Yehova adzachitanso chimodzimodzi ndi maufumu onse amene ali kumene mukuwolokera.+
21 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula Yoswa+ kuti, ‘Iwe ukuona ndi maso zonse zimene Yehova Mulungu wanu wachita ndi mafumu awiriwa. Yehova adzachitanso chimodzimodzi ndi maufumu onse amene ali kumene mukuwolokera.+