Deuteronomo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musalakelake mkazi wa mnzanu.+ Musalakelake mwadyera nyumba ya mnzanu, munda wake, kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ngʼombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzanu.’+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:21 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, ptsa. 21-22 Nsanja ya Olonda,5/15/2012, tsa. 7
21 Musalakelake mkazi wa mnzanu.+ Musalakelake mwadyera nyumba ya mnzanu, munda wake, kapolo wake wamwamuna, kapolo wake wamkazi, ngʼombe yake yamphongo, bulu wake, kapena chinthu chilichonse cha mnzanu.’+