Deuteronomo 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kumeneko muzikapereka nsembe zanu zopsereza, nyama ndi magazi,+ paguwa lansembe la Yehova Mulungu wanu. Magazi a nsembe zanu azidzathiridwa pansi pafupi ndi guwa lansembe+ la Yehova Mulungu wanu, koma nyamayo mungathe kuidya.
27 Kumeneko muzikapereka nsembe zanu zopsereza, nyama ndi magazi,+ paguwa lansembe la Yehova Mulungu wanu. Magazi a nsembe zanu azidzathiridwa pansi pafupi ndi guwa lansembe+ la Yehova Mulungu wanu, koma nyamayo mungathe kuidya.