Deuteronomo 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ukatero uzipereka nsembe zako zopsereza,+ nyama ndi magazi,+ paguwa lansembe la Yehova Mulungu wako. Magazi a nsembe zako uziwathira pansi pafupi ndi guwa lansembe la Yehova+ Mulungu wako, koma nyamayo utha kuidya.
27 Ukatero uzipereka nsembe zako zopsereza,+ nyama ndi magazi,+ paguwa lansembe la Yehova Mulungu wako. Magazi a nsembe zako uziwathira pansi pafupi ndi guwa lansembe la Yehova+ Mulungu wako, koma nyamayo utha kuidya.