Deuteronomo 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zikadzatero Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha, ndipo sadzachitanso chinthu choipa chilichonse ngati chimenechi pakati panu.+
11 Zikadzatero Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha, ndipo sadzachitanso chinthu choipa chilichonse ngati chimenechi pakati panu.+