Deuteronomo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, musaimbe mlanduwu anthu anu Aisiraeli amene munawawombola,+ ndipo musalole kuti mlandu wa magazi a munthu wosalakwa ukhale pa anthu anu Aisiraeli.’+ Akatero iwo sadzaimbidwa mlandu wa magaziwo.
8 Inu Yehova, musaimbe mlanduwu anthu anu Aisiraeli amene munawawombola,+ ndipo musalole kuti mlandu wa magazi a munthu wosalakwa ukhale pa anthu anu Aisiraeli.’+ Akatero iwo sadzaimbidwa mlandu wa magaziwo.