Deuteronomo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati mwapeza chisa cha mbalame mʼmbali mwa msewu kaya chili mumtengo kapena pansi, muli ana kapena mazira, mayi atafungatira ana kapena mazirawo, musamatenge mayi ndi ana omwe.+
6 Ngati mwapeza chisa cha mbalame mʼmbali mwa msewu kaya chili mumtengo kapena pansi, muli ana kapena mazira, mayi atafungatira ana kapena mazirawo, musamatenge mayi ndi ana omwe.+