-
Deuteronomo 22:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Zikatero bambo ndi mayi a mtsikanayo azipititsa umboni wosonyeza kuti mtsikanayo anali namwali kwa akulu a mzinda, kugeti la mzindawo.
-