Deuteronomo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo bambo ndi mayi a mtsikanayo azibweretsa umboni wosonyeza kuti mtsikanayo anali namwali kwa akulu a mzinda kuchipata cha mzindawo.+
15 Pamenepo bambo ndi mayi a mtsikanayo azibweretsa umboni wosonyeza kuti mtsikanayo anali namwali kwa akulu a mzinda kuchipata cha mzindawo.+