Deuteronomo 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova adzachititsa kuti matenda akukakamireni mpaka atakufafanizani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.+
21 Yehova adzachititsa kuti matenda akukakamireni mpaka atakufafanizani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.+