Deuteronomo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amene simukuwadziwa adzadya zipatso zamʼdziko lanu ndi mbewu zanu zonse+ ndipo nthawi zonse muzidzaberedwa mwachinyengo komanso kuponderezedwa.
33 Anthu amene simukuwadziwa adzadya zipatso zamʼdziko lanu ndi mbewu zanu zonse+ ndipo nthawi zonse muzidzaberedwa mwachinyengo komanso kuponderezedwa.