Deuteronomo 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anamuuza kuti: “Ili ndi dziko limene ndinalumbira kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti, ‘Ndidzalipereka kwa mbadwa* zanu.’+ Ndakulola kuti ulione ndi maso ako, koma suwoloka kukalowa mʼdzikolo.”+
4 Ndiyeno Yehova anamuuza kuti: “Ili ndi dziko limene ndinalumbira kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti, ‘Ndidzalipereka kwa mbadwa* zanu.’+ Ndakulola kuti ulione ndi maso ako, koma suwoloka kukalowa mʼdzikolo.”+