-
Yoswa 13:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Malire a fuko la Rubeni anali mtsinje wa Yorodano. Dera limeneli linali cholowa cha anthu a fuko la Rubeni chimene anapatsidwa motsatira mabanja awo. Iwo anapatsidwa derali limodzi ndi mizinda komanso midzi ya kumeneko.
-