Yoswa 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Malire a ana a Rubeni anali mtsinje wa Yorodano. Limeneli ndilo gawo la ana a Rubeni+ limene anapatsidwa potsata mabanja awo. Iwo anapatsidwa mizinda ndi midzi ya kumeneko kuti ikhale cholowa chawo.
23 Malire a ana a Rubeni anali mtsinje wa Yorodano. Limeneli ndilo gawo la ana a Rubeni+ limene anapatsidwa potsata mabanja awo. Iwo anapatsidwa mizinda ndi midzi ya kumeneko kuti ikhale cholowa chawo.