Yoswa 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imeneyi inali mizinda imene inasankhidwa kuti Aisiraeli onse ndi alendo okhala pakati pawo, azithawirako akapha munthu mwangozi,+ kuti asaphedwe ndi wobwezera magazi asanakaonekere pamaso pa oweruza.*+
9 Imeneyi inali mizinda imene inasankhidwa kuti Aisiraeli onse ndi alendo okhala pakati pawo, azithawirako akapha munthu mwangozi,+ kuti asaphedwe ndi wobwezera magazi asanakaonekere pamaso pa oweruza.*+