Oweruza 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho malowo anawapatsa dzina lakuti Bokimu,* ndipo anaperekapo nsembe kwa Yehova.