Oweruza 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho anatcha malowo dzina lakuti Bokimu.* Ndipo anapereka nsembe kwa Yehova pamalowo.