-
Oweruza 6:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mngelo wa Mulungu woona anamuuza kuti: “Tenga nyamayi ndi mikateyo nʼkuziika pamwala waukuluwo, ndipo ukhuthule msuziwo.” Gidiyoni anachitadi zomwezo.
-