Oweruza 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo mngelo wa Mulungu woona anamuuza kuti: “Tenga nyamayi ndi mikate yopanda chofufumitsayo, ndi kuziika pamwala waukuluwo,+ ndipo ukhuthule msuziwo.” Gidiyoni anachitadi zomwezo.
20 Pamenepo mngelo wa Mulungu woona anamuuza kuti: “Tenga nyamayi ndi mikate yopanda chofufumitsayo, ndi kuziika pamwala waukuluwo,+ ndipo ukhuthule msuziwo.” Gidiyoni anachitadi zomwezo.