-
Oweruza 6:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno anayamba kufunsana kuti: “Ndani wachita zimenezi?” Atafufuza ananena kuti: “Wachita zimenezi ndi Gidiyoni, mwana wa Yowasi.”
-