-
Oweruza 6:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno anayamba kufunsana kuti: “Ndani wachita zimenezi?” Choncho anayamba kufufuza ndi kufunafuna amene anachita zimenezo. Pamapeto pake iwo anati: “Ndi Gidiyoni, mwana wa Yowasi amene wachita zimenezi.”
-