Oweruza 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero amuna a mumzindawo anauza Yowasi kuti: “Bweretsa mwana wako timuphe, chifukwa wagwetsa guwa lansembe la Baala nʼkudula mzati wopatulika* umene unali pambali pake.”
30 Zitatero amuna a mumzindawo anauza Yowasi kuti: “Bweretsa mwana wako timuphe, chifukwa wagwetsa guwa lansembe la Baala nʼkudula mzati wopatulika* umene unali pambali pake.”