Oweruza 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo amuna a mumzindawo anauza Yowasi kuti: “Tulutsa mwana wako kuti timuphe,+ chifukwa wagwetsa guwa lansembe la Baala ndi kudula mzati wopatulika umene unali pambali pake.”
30 Pamenepo amuna a mumzindawo anauza Yowasi kuti: “Tulutsa mwana wako kuti timuphe,+ chifukwa wagwetsa guwa lansembe la Baala ndi kudula mzati wopatulika umene unali pambali pake.”