-
Oweruza 7:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Atatero magulu atatuwo analiza malipenga a nyanga ya nkhosa nʼkuphwanya mitsuko ikuluikulu ija. Ananyamula zounikira kudzanja lawo lamanzere ndipo ankaliza malipenga omwe anali kudzanja lawo lamanja, nʼkuyamba kufuula kuti: “Nkhondo ya Yehova komanso ya Gidiyoni!”
-