Oweruza 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa nthawi yonseyi nʼkuti aliyense ataimirira pamalo ake kuzungulira msasawo ndipo asilikali onse a Amidiyani anayamba kuthawa kwinaku akufuula.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:21 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, tsa. 31
21 Pa nthawi yonseyi nʼkuti aliyense ataimirira pamalo ake kuzungulira msasawo ndipo asilikali onse a Amidiyani anayamba kuthawa kwinaku akufuula.+