Oweruza 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa nthawi imeneyi aliyense anaimirirabe pamalo ake kuzungulira msasa wonsewo, ndipo mumsasa wonse wa Amidiyani munali chipwirikiti, anthu anali kufuula ndi kuthawa.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:21 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, tsa. 31
21 Pa nthawi imeneyi aliyense anaimirirabe pamalo ake kuzungulira msasa wonsewo, ndipo mumsasa wonse wa Amidiyani munali chipwirikiti, anthu anali kufuula ndi kuthawa.+