-
Oweruza 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ali mʼnjira, anagwira mnyamata wa ku Sukoti nʼkuyamba kumufunsa mafunso. Mnyamatayo analembera Gidiyoni mayina okwana 77 a akalonga ndi akulu a ku Sukoti.
-