Oweruza 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali m’njira, anagwira mnyamata wa ku Sukoti+ amene anam’funsa mafunso.+ Pamenepo, mnyamatayo analembera Gidiyoni mayina okwana 77 a akalonga+ ndi akulu a mzinda wa Sukoti.
14 Ali m’njira, anagwira mnyamata wa ku Sukoti+ amene anam’funsa mafunso.+ Pamenepo, mnyamatayo analembera Gidiyoni mayina okwana 77 a akalonga+ ndi akulu a mzinda wa Sukoti.