Oweruza 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde funsani atsogoleri* onse a ku Sekemu kuti, ‘Chabwino nʼchiyani kwa inu, kuti ana onse 70 a Yerubaala+ azikulamulirani, ndi kuti azikulamulirani munthu mmodzi? Ndipo musaiwale kuti ine ndi inu ndife magazi amodzi.’”*
2 “Chonde funsani atsogoleri* onse a ku Sekemu kuti, ‘Chabwino nʼchiyani kwa inu, kuti ana onse 70 a Yerubaala+ azikulamulirani, ndi kuti azikulamulirani munthu mmodzi? Ndipo musaiwale kuti ine ndi inu ndife magazi amodzi.’”*