Oweruza 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde lankhulani nzika zonse za Sekemu zikumva, kuti, ‘Chabwino n’chiti kwa inu, kuti amuna 70,+ ana onse a Yerubaala akulamulireni, kapena munthu mmodzi akulamulireni? Ndipotu kumbukirani kuti ine ndine fupa lanu ndi mnofu wanu.’”+
2 “Chonde lankhulani nzika zonse za Sekemu zikumva, kuti, ‘Chabwino n’chiti kwa inu, kuti amuna 70,+ ana onse a Yerubaala akulamulireni, kapena munthu mmodzi akulamulireni? Ndipotu kumbukirani kuti ine ndine fupa lanu ndi mnofu wanu.’”+