-
Oweruza 9:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma mtengo wa mkuyuwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kukoma kwanga ndi zipatso zanga zabwinozi nʼkupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’
-