Oweruza 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma mtengo wa mkuyuwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kukoma kwanga ndi zipatso zanga zabwinozi, n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’+
11 Koma mtengo wa mkuyuwo unayankha kuti, ‘Kodi ndisiye kukoma kwanga ndi zipatso zanga zabwinozi, n’kupita kuti ndizikagwedezeka pamwamba pa mitengo ina?’+