-
Oweruza 9:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho, atsogoleri a ku Sekemu anatumiza anthu kuti akamubisalire pamwamba pa mapiri, ndipo anthuwo ankalanda katundu munthu aliyense wodutsa njira imeneyo. Patapita nthawi, Abimeleki anauzidwa zimenezi.
-