-
Oweruza 9:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho, nzika za Sekemu zinamuikira obisalira anthu pamwamba pa mapiri kuti amuvulaze, ndipo obisalira anthuwo anali kulanda katundu wa munthu aliyense wodutsa njira imeneyo. Patapita nthawi, Abimeleki anauzidwa zimenezi.
-