-
Oweruza 9:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Choncho anatumiza anthu mobisa kuti akauze Abimeleki kuti: “Gaala mwana wa Ebedi ndi abale ake abwera ku Sekemu ndipo akulimbikitsa anthu amumzindawu kuti akuukireni.
-