Oweruza 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho anachitira chinyengo Gaala ndi kutumiza mithenga kwa Abimeleki kuti: “Gaala mwana wa Ebedi pamodzi ndi abale ake alowa mu Sekemu+ ndipo akulimbikitsa anthu a mumzindawu kuti akuukireni.
31 Choncho anachitira chinyengo Gaala ndi kutumiza mithenga kwa Abimeleki kuti: “Gaala mwana wa Ebedi pamodzi ndi abale ake alowa mu Sekemu+ ndipo akulimbikitsa anthu a mumzindawu kuti akuukireni.