-
Oweruza 9:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Patapita nthawi Gaala ananenanso kuti: “Taona, anthu akubwera kuchokera chapakati apo, ndipo gulu limodzi ladzera njira yodutsa kumtengo waukulu wa Meyonenimu.”
-