Oweruza 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zitatero, Gaala ananenanso kuti: “Taona, anthu akubwera chakuno kuchokera pakati pa dziko, ndipo gulu limodzi likubwera kudzera njira yodutsa ku mtengo waukulu wa Meyonenimu.”*
37 Zitatero, Gaala ananenanso kuti: “Taona, anthu akubwera chakuno kuchokera pakati pa dziko, ndipo gulu limodzi likubwera kudzera njira yodutsa ku mtengo waukulu wa Meyonenimu.”*