Oweruza 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zebuli anamuyankha kuti: “Suja umadzitama kuti, ‘Abimeleki ndi ndani kuti tizimutumikira?’+ Amenewa si anthu amene unawakana aja? Ndiyetu pita ukamenyane nawo.”
38 Zebuli anamuyankha kuti: “Suja umadzitama kuti, ‘Abimeleki ndi ndani kuti tizimutumikira?’+ Amenewa si anthu amene unawakana aja? Ndiyetu pita ukamenyane nawo.”