Oweruza 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamenepo Zebuli anamuuza kuti: “Kodi waiwala mawu ako aja amene unanena+ kuti, ‘Abimeleki ndani, kuti timutumikire?’+ Kodi amenewa si anthu amene unawakana?+ Ndiyetu pita, ukamenyane nawo.”
38 Pamenepo Zebuli anamuuza kuti: “Kodi waiwala mawu ako aja amene unanena+ kuti, ‘Abimeleki ndani, kuti timutumikire?’+ Kodi amenewa si anthu amene unawakana?+ Ndiyetu pita, ukamenyane nawo.”