Salimo 94:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+ Miyambo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+ Yakobo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.
4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+
5 N’chimodzimodzinso lilime. Lilime ndi kachiwalo kakang’ono, koma limadzitama kwambiri.+ Tangoganizani mmene kamoto kakang’onong’ono kamayatsira nkhalango yaikulu.