-
Oweruza 9:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Abimeleki anayamba kuthamangitsa Gaala, ndipo Gaala anathawa. Anthu ambiri anaphedwa ndipo mitembo inali paliponse mpaka kukafika kugeti la mzinda.
-