-
Oweruza 9:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Pamenepo Abimeleki anathamangitsa Gaala, ndipo Gaala anathawa. Anthu ochuluka anaphedwa ndipo mitembo inali paliponse mpaka kukafika kuchipata cha mzinda.
-