-
Oweruza 9:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Abimeleki ndi magulu amene anali nawo anathamanga nʼkukaima pageti la mzinda, pamene magulu awiri anathamangira kwa anthu amene anali kunja kwa mzinda, ndipo anayamba kuwapha.
-