Oweruza 9:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Abimeleki ndi magulu amene anali nawo anathamanga kuti akaime pachipata cha mzinda, pamene magulu ena awiri anathamangira kwa anthu amene anali kunja kwa mzinda, ndipo anayamba kuwakantha.+
44 Abimeleki ndi magulu amene anali nawo anathamanga kuti akaime pachipata cha mzinda, pamene magulu ena awiri anathamangira kwa anthu amene anali kunja kwa mzinda, ndipo anayamba kuwakantha.+