-
Oweruza 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma Yefita anawauza kuti: “Ineyo ndi anthu anga tinalimbana koopsa ndi Aamoni. Ndinakuitanani kuti mudzandithandize koma simunandipulumutse mʼmanja mwawo.
-